KuswaKuswa

KuswaKuswa Kwao kwachilungamo ndikuno.

27/08/2026

Chili pamuna ndondoondoo

24/08/2026

Kuli page Ya FATIMA ku Tiktok 💔😭🙌,
Akuvala ngt msilamu koma ma caption kumuposa satana😫😫..

24/08/2026

Kumangochi kwagwa mulili�����,

Ati adikila lithe zezeni

21/08/2026

Ndili ndi Sate saka! Eyetu🫠😆...

Anyway mpatseni cross iyi Abdul Rasheed 🤣🙌

Umh anyway! Nikkah Mubarak ❤️🙌Abdul Rasheed Nanga izi ndi zovuta? 😅😂🤣🤣
20/08/2026

Umh anyway! Nikkah Mubarak ❤️🙌
Abdul Rasheed Nanga izi ndi zovuta? 😅😂🤣🤣

18/08/2026

Chisilamu kuzati:
سِبَابُ الْمُسْلِمِ فُسُوقٌ، وَقِتَالُهُ كُفْرٌ
Sahih Al-Bukhar

Atsikana athuwo kuchita k*tukwana NCHIZUNGU💔🙌,
akuonetsa k*t amaimva kukoma nyimboyo, Kaya chizungucho sanachimve kt ndi phuzo.. Zosawakhala🙌,

Batchala kuikila umboni🤣 Mboni Yosakwatila😂🤣🙌..
18/08/2026

Batchala kuikila umboni🤣
Mboni Yosakwatila😂🤣🙌..

14/08/2026

Umh! 🙌
Nkhosa zandaniso izi!? 🤔💔

Pamene ak*tulutsa Nasheed ya MAFUNSO ANGA, nafeso Tilindi MAFUNSO athu kwa nyamata OMETA M'baliliyi! Eni mudzi mulibe MA...
11/08/2026

Pamene ak*tulutsa Nasheed ya MAFUNSO ANGA, nafeso Tilindi MAFUNSO athu kwa nyamata OMETA M'baliliyi! Eni mudzi mulibe MAFUNSO anu? 😅😂😂

Tieni tidikile uthenga okhao basi, zinazo mzake

04/08/2026

Ma Artist a Deen ACHAMBA? 😳🙆
zatipatsa mantha😱🙌

Address

92 Xavier Street, Robertsham
Blantyre
2091

Telephone

+265881212646

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KuswaKuswa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share